|
1. Unsembe umodzi mwa
Yesu
Paubatizo wawo akazi ndio amuna amasanduaka atumuki ofanana mu
unsembe wa Khristu. Kufananaku kuli chimodzimozdi pa kudzodzedwa
unsembe. click!
2. Apatsidwa mphamvu ya
kutsogelera
Pa khomaliro otsiliza Khrist anapreka mphamvu mofanana kwa amai ndi
abambo. Choncho onsewa atha kulandira mphmvu zosandulitsa ukalistia.
click!
3. Chikkalidwe cha mafuko cha
tsamkho Chizolowezi choletsa amai kudzodzedwa unsembe chidambika ndi tsakho
lomwe linali ndi mbali zitatu. Tankholi lidapotoza kuganiza kwa a tsogoleri a
mp[ingo pa nkhaniyi. click!
4. Amayi akhala ma
dikoni Pachiyambi mpaka chaka cha 900 Mpingo umapereka undindo wosapereweza
kwa amayi osanduliza ukalistia podzodza amayi u dikoni. Iziti
zikusonyeza kuti mayi athanso kudzodzedwa unsembe. click!
5. Zoyenertsa mai kudzodwa
unsembe zakhala zilipo nthawi yomwe mpingo udali nchizolowezi cha
chete. Mwachitsanzo chizolewesi cholemeza amayi Maria ngati wansembe. Izitu
zikutanthuza kuti, naga 'mkulingalira kwa akhristu', It shows that, according
to the sense of the faithful, kudzera mchitsanzo cha amayi Maria
mtsakho lotchingiriza amayi ku unsembe ndi longonjetsedwa kale.click!
6. A Khristu amabiri mziko
lapansi amavomereza unsembe wa amayi.
Pambuyo pa kusinkhasinkha ndi ma mapepmhero a Kristu a mpipingo ina
amadzodza mai oyenerera unsembe. Ngakhale kuti si zonse zomwe mipingo ina
imachita nzovomerezeka kwa akatolika, zimvano cha a khristu a mpipingo ya mbiri
pa unsembe wa amayi sikutsindika mfundo unsembe wa amai ngolingana ndi
chifuniro cha Khristu.click!
7. Amayinso, ponena mwa
tchutchutchu, ngoitanidwa ku unsembe.
Popeza kuti amayi ambiri wodzilemekeza amamva mu mtima mwawo
kuitanidwa ku unsembe izi nzisoneza za chifunuiro cha Mzimu Woyera chomwe ife
sitiyenera kuchikana.click!
Po tsiliza: palibe
zenizeni mwa mfundo zomwe zimaperekedwa pa tsankho lomwe limarepheretsa
ami kulowa unsembe, ndiponso mfumdo zambirizogwirizana chikhululupiriro cha
chikatolika zikukomera maganizo a unsembe wa amayi! |