Chichewa UNSEMBE WE AMAYI
header

Responsive image
HOME REASONS DEFY THE POPE?! DEBATE MENU
Nederlands/Vlaams Deutsch Francais English language Spanish language Portuguese language Catalan Chinese Czech Malayalam Finnish Igbo
Japanese Korean Romanian Malay language Norwegian Swedish Polish Swahili Chichewa Tagalog Urdu
------------------------------------------------------------------------------------
Mfundo

Pali pafufupi mfundo zizanu ndi ziwiri yeneretsa amayi kudzodzedwa Unsembe

1. Unsembe umodzi mwa Yesu
Paubatizo wawo akazi ndio amuna amasanduaka atumuki ofanana mu unsembe wa Khristu.
Kufananaku kuli chimodzimozdi pa kudzodzedwa unsembe.
click!

2. Apatsidwa mphamvu ya kutsogelera
Pa khomaliro otsiliza Khrist anapreka mphamvu mofanana kwa amai ndi abambo. Choncho onsewa atha kulandira mphmvu zosandulitsa ukalistia. click!

3. Chikkalidwe cha mafuko cha tsamkho
Chizolowezi choletsa amai kudzodzedwa unsembe chidambika ndi tsakho lomwe linali ndi mbali zitatu. Tankholi lidapotoza kuganiza kwa a tsogoleri a mp[ingo pa nkhaniyi. click!

4. Amayi akhala ma dikoni
Pachiyambi mpaka chaka cha 900 Mpingo umapereka undindo wosapereweza kwa amayi osanduliza ukalistia podzodza amayi u dikoni. Iziti zikusonyeza kuti mayi athanso kudzodzedwa unsembe. click!

5. Zoyenertsa mai kudzodwa unsembe zakhala zilipo nthawi yomwe mpingo udali nchizolowezi cha chete.
Mwachitsanzo chizolewesi cholemeza amayi Maria ngati wansembe. Izitu zikutanthuza kuti, naga 'mkulingalira kwa akhristu', It shows that, according to the ‘sense of the faithful’, kudzera mchitsanzo cha amayi Maria mtsakho lotchingiriza amayi ku unsembe ndi longonjetsedwa kale.click!

6. A Khristu amabiri mziko lapansi amavomereza unsembe wa amayi.
Pambuyo pa kusinkhasinkha ndi ma mapepmhero a Kristu a mpipingo ina amadzodza mai oyenerera unsembe. Ngakhale kuti si zonse zomwe mipingo ina imachita nzovomerezeka kwa akatolika, zimvano cha a khristu a mpipingo ya mbiri pa unsembe wa amayi sikutsindika mfundo unsembe wa amai ngolingana ndi chifuniro cha Khristu.click!

7. Amayinso, ponena mwa tchutchutchu, ngoitanidwa ku unsembe.
Popeza kuti amayi ambiri wodzilemekeza amamva mu mtima mwawo kuitanidwa ku unsembe izi nzisoneza za chifunuiro cha Mzimu Woyera chomwe ife sitiyenera kuchikana.click!

Po tsiliza: palibe zenizeni mwa mfundo zomwe zimaperekedwa pa tsankho lomwe limarepheretsa ami kulowa unsembe, ndiponso mfumdo zambirizogwirizana chikhululupiriro cha chikatolika zikukomera maganizo a unsembe wa amayi!

Join us  .  .  .  !

Nanganso bwanji uphunzi wa a Papa
ukutchingiriza unsembe wa a mayi?

Werengani mafunso amene amabwera pafupipafupi!
Zina
Wijngaards Institute for Catholic ResearchThis website is maintained by the Wijngaards Institute for Catholic Research.

The Institute is known for issuing academic reports and statements on relevant issues in the Church. These have included scholars' declarations on the need of collegiality in the exercise of church authority, on the ethics of using contraceptives in marriage and the urgency of re-instating the sacramental diaconate of women.

Visit also our websites:Women Deacons, The Body is Sacred and Mystery and Beyond.

You are welcome to use our material. However: maintaining this site costs money. We are a Charity and work mainly with volunteers, but we find it difficult to pay our overheads.


Visitors to our website since January 2014.
Pop-up names are online now.The number is indicative, but incomplete. For full details click on cross icon at bottom right.


Please, support our campaign
for women priests
Join our Women Priests' Mailing List
for occasional newsletters:
Email:
Name:
Surname:
City:
Country:
 
An email will be immediately sent to you
requesting your confirmation.