Unsembe wa Amayi

Zifukwa zodzodzera Amayi Unsembe mu tchalitchi la Katolika

Nkhani ndi mabuku pa internetemail us
Unsembe Umodzi mwa Khiristu

Unsembe umodzi mwa Khristu

Background music?

Zzikukwa zisanu m’mziwiri zoyambirira zoti amayi ngoyera kudzodzedwa Unsembe

Nchipangano Chakale anthu wakazi samawerengerenga ngati anthu monga anthu wamuna. Popeza amayi samkaumbala samawerengedwa ngati anthu osankhidwa ndi Mulungu. Choncho amayi analibe ufulu wopereka msembe zao paokha. Thawi zonse ntchito zao pa zachipembedzo zimakhala zongothandiza amuna omwe ankawapondereza.

The mystery of baptism Ambuye Yesu anasudzula nchitidwe wopondreza amayi
Mzimayi aliyense wobatizidwa amasanduka chifanizo cha Ambuye Yesu, chimodzimodzi mu ubatizo wa amuna. ““Onse amene abatizidwa mwa Khristu, atengere chifanizo cha Khristu. Palibenso tsankho pakati pa Ayuda ndi anthu ena onse, kapolo ndi mfulu, mamuna ndi mkazi .” Galatians 3,28
Choncho mkazi aliyense wobatizidwa amatenga mbali mopanda kutsaliza mu unsembe wa Khristu, mu utumiki wake mu ufumu ndi ulaliki.

Ubatizo ndi mphatso yomwe yimatiyeneretsa kulandira masakramenti onse, ndi unsembe omwe.
Zina?

1 2 3 4 5 6 7
obatizidwa olimbikitsidwa omasulidwa odzodzedwa ovomerezedwa othandizika oitanidwaThis website is maintained by the Wijngaards Institute for Catholic Research.

See our Documented Appeal to Pope Francis to Request the Re-instatement of the Ordained Diaconate for Women.

Wijngaards Institute for Catholic Research

Dear visitor, you are welcome to use our material. However: building up and maintaining this site costs money. We are a Charity and work mainly with volunteers, but find it difficult to pay our overheads. Please, become a Friend or support us with a donation. Also, as some of you recommended to us, we are exploring how to generate income by advertising. Please, support us in this effort and send us your suggestions.
John Wijngaards

Wijngaards Institute for Catholic Research

Miriam Duignan


Please, support our campaign
for women priests

Visit our new websites:

Natural Law and Conscience

Synod on the Family 2015

Catholics and Contraception

Join our Women Priests' Mailing List
for occasional newsletters:
Email:
Name:
Surname:
City:
Country:
 
An email will be immediately sent to you
requesting your confirmation.