Unsembe wa Amayi

Zifukwa zodzodzera Amayi Unsembe mu tchalitchi la Katolika

Nkhani ndi mabuku pa internetemail us
Tamasuludwa ku Tsankho

Tamasuludwa ku Tsankho

Background music?

Zoonadi, kalelo Mpingo unkakana kudzodza amayi kuti akhale ansembe.
Koma chifukwa?
Polingalira machitidwe a mpingo kalelo, tiyeneranso kufufuza zifukwa zoyenra zomwe anthu ankaganira kuti amayi asakhale ansembe. Chifukwa chiyani amai samadzodzedwa unsembe
Koma kwa amayi, akafufuza amaona kuti zifukwazi nzokhumudwitsa.
Amayi ankakanizidwa kulowa unsembe pazifukwa zopanda pake.

The evil of prejudice Mfundo zitatu zopondereza zimalepheretsa amayi kutumikira muunsembe.

1. 1. Amayi ankaonebwa ngati otsalira mu zonse: mphamvu za thupi, mu mzeru ndi mu kulimba mtima.
Amkatero popeza ankakhulupira kuti ku mbewu yomwe imabweretsa mwa wa mamuna ‘mwakhazikitsidwa’ chimanga mtundu, choncho amayi ankaonedwa ngati anthu operewedwa.
Machdule, Amayi ankatengedwa ngat anthu operewedwa.

2. Popeza Eva adagwetsa mtundu wa anthu, mkazi aliyense ankaganiziridwa kuti ali ndi themebrero la Eva.
Women were marked as sinful creatures.

3. Anthu amaganiza kuti mayi akakhala akasamba ndiye kuti ndiwodetsedwa.
Poonedwa ngati anthu odetsedwa amayi samaloredwa kutenga mbali pa mwambo wothira msembe


  Nthawi zonse Mpingo usowa kudzimasula mu mtcichidwe wa tsankho womwe umaonengwa ziphunzitso ndi zizolewezi zabwino mu mpingo.

Kufikira m’chaka cha 1854 a Papa amkaphunzitsa kuti ukapolo ngovomerezeka kwa Mulungu, koma tsopano Mpingo umaletsa ukapolo.

The Church has made many similar mistakes throughout its history.

Amayi a lero ayenera kumasulidwa mu la chimpunzitso cha tsankho mu mpingo chomwe chimaletsa amayi kutenga mbali mu utumiki wa unsembe umene Mulungu adawaitainira.
 
    Zina
1 2 3 4 5 6 7
obatizidwa olimbikitsidwa omasulidwa odzodzedwa ovomerezedwa othandizidwa oitanidwaThis website is maintained by the Wijngaards Institute for Catholic Research.

See our Documented Appeal to Pope Francis to Request the Re-instatement of the Ordained Diaconate for Women.

Wijngaards Institute for Catholic Research

Dear visitor, you are welcome to use our material. However: building up and maintaining this site costs money. We are a Charity and work mainly with volunteers, but find it difficult to pay our overheads. Please, become a Friend or support us with a donation. Also, as some of you recommended to us, we are exploring how to generate income by advertising. Please, support us in this effort and send us your suggestions.
John Wijngaards

Wijngaards Institute for Catholic Research

Miriam Duignan


Please, support our campaign
for women priests

Visit our new websites:

Natural Law and Conscience

Synod on the Family 2015

Catholics and Contraception

Join our Women Priests' Mailing List
for occasional newsletters:
Email:
Name:
Surname:
City:
Country:
 
An email will be immediately sent to you
requesting your confirmation.