Unsembe wa Amayi

Zifukwa zodzodzera Amayi Unsembe mu tchalitchi la Katolika

Nkhani ndi mabuku pa internetemail us

Kuitanidwa ndi Mzimu Woyera

Background music?

Maziko a mkuitanidwa ku moyo uliwonse ali amafumira moti tinalenngedwa ndi Mulungu. Mphatso zathu zonse timalandira kuchokera m’manja mwa Mulungu chomwechonso kuitanidwa kwathu, kaya mkuntchito, ku utumiki kapenaso ku ntchito yokatumikira mafuko ena, zonsensi zimatheka popeza Mulungu amatiitana ife amene sitinali kathu mkomwe potisandutsa ana a Mulungu.


Chomwechonse tikalingalira utumiki wa unsembe, Mpingo wakhala ukukhulupirira kuti .As to priestly vocations, there has always been a conviction within the Church that kuitanidwa koona kumachokera kwa Mulungu, , choncho ndi upandu waukulu kutchingiriza amayi kutenga mbali ku utumikiwu.

Women are called to holy oders! Ponena mwa mosapsyatira pali umboni woti amayi ambiri a Chikatolika, mziko lonse lapansi, amagundidwa mu mtima kuti Mulungu akuwaitanira ku unsembe.

Werengani za umboni wa amai a lero womwe mu mtimwa mwawo akumva kuitanidwa ku unsembe.

Kalero kuitanidwa kwa amayi ku unsembe, nthawi zambiri, kumatchingirizidwa ndi chikhalidwe cha tsankho cha mafuko a anthu. Ngakhale zinali cnoncho, tili ndi zitsanzo za mbiri za amayi Woyera amene anavomera kuitanidwa ku utumukiwu:
Katalina woyera wa ku Siena, Dotoro wa mtchalitchi
Tereza Woyera wa ku Lisieux, Dotoro wa mtchalitchi

ndi wena ambiri.

Zotsatira za kafukufuku ofufuza maganizo a amayi 100 omwe anamva kuitainidwa ku unsembe m’mitima mwawo zikusonyeza kuti amayiwa ali ndi luntha, ndi wodzipereka ndiponso woyenera unsembe monga amuna onse amene amamva kuitananidwaku Werengani pano.


  Kudzera mu kugunda mu mtima mwa amayi a Chikatolika omwe ndi oyinanidwa ku kuunsemmbe Mzimu Woyera ukupempha Mpingo kuti uwunikirenso pa za mtsankho lomwe limalepheretsa amayi kulowa unsembe.

Mu mpingo mpaka padzakhale kusintha tikapanda kumva kugunda kwa Mzimu Woyera mtimima ya amayi, ntchito za mpingo zimanidwa mphatso za mtengo wapatali zomwe Mzimu Woyera wapereka kwa Amayi.
 
    Return to preasons
1 2 3 4 5 6 7
obatizidwa olimbikidwa omasulidwa odzodzedwa ovomerezedwa othandizidwa oyitanidwaThis website is maintained by the Wijngaards Institute for Catholic Research.

See our Documented Appeal to Pope Francis to Request the Re-instatement of the Ordained Diaconate for Women.

Wijngaards Institute for Catholic Research

Dear visitor, you are welcome to use our material. However: building up and maintaining this site costs money. We are a Charity and work mainly with volunteers, but find it difficult to pay our overheads. Please, become a Friend or support us with a donation. Also, as some of you recommended to us, we are exploring how to generate income by advertising. Please, support us in this effort and send us your suggestions.
John Wijngaards

Wijngaards Institute for Catholic Research

Miriam Duignan


Please, support our campaign
for women priests

Visit our new websites:

Natural Law and Conscience

Synod on the Family 2015

Catholics and Contraception

Join our Women Priests' Mailing List
for occasional newsletters:
Email:
Name:
Surname:
City:
Country:
 
An email will be immediately sent to you
requesting your confirmation.