Unsembe wa Amayi

Zifukwa zodzodzera Amayi Unsembe mu tchalitchi la Katolika

Nkhani ndi mabuku pa internetemail us
Anadzodzedwa ngati ma Dikoni

Anadzodzedwa ngati ma Dikoni

Background music?

tikatsatiza mbiri ya MpingoIn the course of the Church’s history, ntchito zitatu za utumiki zasanduka ntchito zomwe anthu okhaokha odzodzedwa amagwira .
Izi mzomwe nthawi zina zimadziwika ndikuti sacramenti la unsembe.
Mchikatolika tikuzidziwa ngati u episikopi, unsembe ndi udikoni.
Ngakhale kuti ma udindo ngosiyana, ntcito zitatu zonsezi nzogwiranaThough different in scope, all three are part of musakramenti limodzi la ukulu mu unsembe.

Nsonkhano wachiwiri wa ku Vatikani unakambiranaumodzi wa utumiki 'wochekera kwa Mulungu umene umagawika mu utumiki utaku umene kuchokera pa chiyambi umadzika ndi kuti ma bishopi, ansembe ndi ma dikoni'(Lumen Gentium § 28).

Women were ordained deacons! A mayi anankadzodzedwa u dikoni pa chiyambi cha mpingo.

Za mchitidwewu zinalembedwa m'mabukuomwe anafalikira ku malo ambiri pafufupi zaka 900 makamaka mu Mpingo wa mbali ya ku mwera.

Ma dikoin a akazi anali ofunika Women deacons assisted pa ubatizo wa amayi mwambo womwe mai amamizidwa m'madzi pobatiziwa.

Tikudzewa za mwambo weniweni womwe ankatsatiza podzodza amayi. A Bishopi ankawasanja manja pa mutu ndipo ankapempha Mzimu Woyera kuti awatsikire ndi madalitso ndiponso ankawaveka sitolo ya u dikoni khosi mwawo.
Pano werengani chitsanzo cha mwambo umenewu.

Padalibe kusiyana pa kudzodzedwa u dikoni kwa a mayi ndi abanmbo popeza anali ndi utumiki wofanana. Ngati pamkakhala zina zokwanira zolepheretsa amayi kudzedwa u dikoni, zomwezo zinkalepheretsa abambo kulowa mu udikoni.


  Chigawo cha ku m'mawa cha mpingo wa Katolika pa nthawiyo chinali monnga ulili Mpingo wa Katolika popeza kugawikana (Eastern Rite) kudabwera mchaka cha 1054..

Chitanzo china chioneka tikatsata utumiki wa Paulo woyera yemwe ankagwirira ncthito limomdzi ndi mayi waotchedwa Febe (Phoebe) ku Cenchreae, ‘awa anli a Dikoni a Mpingo wa ku Cenchreae’ (Romans 16,1-2).

Ma Kansolo a mpingo oyimira maiko angapo, monga Chalcedon, Trullo and Nicaea II anavomereza za kudzodza amai unsembe.


Ngati amayi ankalandira Sacramenti la Unsembe pa nethawi imeneyo, alakeranji kudzodwa nthwi zino.

 

Buku lo kamaba za u dikoni wa amayi lomwe lasindikizidwa posachedwapa
Palibe malo Amayi mu Sakramenti la Unsembe? A Dikoni a akazi a kalekale
woledwa ndi John Wijngaards, Canterbury Press 2002.

"Ili ndi buku lolebwedwa mwa luso lomwe latsatiza mbiri ya mpingo mozama ndipo mogwira mtima, lolembedwa ndi mlembi yemwe amadziwa nkhawa zomwe akhristu alinazo mu mtima polingalira mtsankho lomwe limatchingiriza amayi kulowa unsembe . A Wijngaards agwiranso ntchito yapamwamba potanthauzira makalata akale omwe munalembedwa mbiri ya mpingo kuti anthu onse athe wodziwerengera paokha."

Script for dramatizing the ancient ordination rite

Reviews ----- * ----- How to Order

    Zina?

1 2 3 4 5 6 7
Kubatizidwa Kulimbikitsidwa Kumasulidwa Kudzodedwa Kuvomerezedwa Kuthandizidwa KuitanidwaThis website is maintained by the Wijngaards Institute for Catholic Research.

See our Documented Appeal to Pope Francis to Request the Re-instatement of the Ordained Diaconate for Women.

Wijngaards Institute for Catholic Research

Dear visitor, you are welcome to use our material. However: building up and maintaining this site costs money. We are a Charity and work mainly with volunteers, but find it difficult to pay our overheads. Please, become a Friend or support us with a donation. Also, as some of you recommended to us, we are exploring how to generate income by advertising. Please, support us in this effort and send us your suggestions.
John Wijngaards

Wijngaards Institute for Catholic Research

Miriam Duignan


Please, support our campaign
for women priests

Visit our new websites:

Natural Law and Conscience

Synod on the Family 2015

Catholics and Contraception

Join our Women Priests' Mailing List
for occasional newsletters:
Email:
Name:
Surname:
City:
Country:
 
An email will be immediately sent to you
requesting your confirmation.