Category: Chichewa

Maphunzitso a Mpinngo wosatsutsika?

Maphunzitso a Mpinngo wosatsutsika?

“Zoonadi!

Bungwe akatswiri pa Chiphunzitso cha chikhulupiriro chathu lagamula kuti nkhani ya unsembe wa amayi ndi chiphunzitso chosasinthika!!!

a Kadinolo Ratzinger, Mtsogoleri wolamulira Bungwe la akatswiri pa za Malamulo woyera a Mpingo anati: ‘nkhani zokambirana unsembe wa amayi zamangika popeza nkhaniyi yalowa mu ziphunzitso zosatsuka za mpingo kudzera nchilamulo cha Aphunzitsi akulu a Mpingo. ”
Response to a Doubt, 28 October 1995

“Anaterodi? Kuletsa nkhayini, komadi?

A ‘Phunzitsi akulu a Mpingo a dziko lonse la pansi' amayimira chiphunzitso ndi maganizo a ma Bishopi onse a Dziko la pansi.

Komano a Bishopi onse pamodzi sanagwirizanepo chiphunzitso chioletsa kupitiriza kukambirana unsembe wa Amayi.”

“Tayambani mwaima kaye!

Pali unyinji ma Bishopi a dziko la pansi omwe amakhulupirira kuti amayi sangadzodzedwe unsembe.

Izi nzachidziwikire chifukwa ambiri mwa ma Bishopiwa anasankhidwa chifukwa amagwirizana ndi maganizo a Papa pa nkhani ya unsembe wa Amayi!”

“Tiyeni tiunikirenso nkhaniyi!

Mkutheka kuti mabishopi onse a dziko la pansi amakhupirira kuti amayi siwoyenera kulowa unsembe. Chigwirizano choterechi chimaziwika ndi mau akuti opinio communis (maganizo ogwirizana).

Opinio communis Komano poyang'anira mbiri ya Mpingo tiona kuti chigwirizano cha maganizo a ma Bishopi chithanso kukhala ndi zolakwika.

Zaka 100 zapitazo ma bishopi ambiri amatsutsa maphunziro a Sayansi omwe amalongosola za mayambiriro a chilengedwe cha anthu. Nthawi imeneyo panali chikhupiriro chozama choti dziko linalenedwa m'masiku asanu ndi limodzi! Izi sizikutanthauza kuti ma Bishopi onse umagwirizana pa umphunzitsi umenewu.

“Nanga chimapangitsa kuti nkhani ikhale uphunzitsi wa ma Bishopi mogwirizana wogwizana ndi chiyani?

Kodi nsonkhano waukulu wachiri ku Vatikani sudagwirizana kuti: ‘Ma Bishopi, pamozdi ndi a Papa, monga a phunzitsi akulu mu Mpingo ayenera kulemekezedwa ndi aKhristu onse monga atetezi achifuniro cha Mulungu mu tchalitchi la Katolika?
Lumen Gentium § 25b.

“Chabwio, tiyeni tiwerengwe ndime yonse ya nkhaniyi!

Nsonkhano wachiwitri ku Vatikani udati: ‘ Ma Bishops angathe kulamula kuti maphunziro Khristu ndi wosatsutsika, nthawi ina iliyonse pomwe, ngakhale atakhala malo osasiyansiyana, pokhapokhapo ngati maganizo awo ngogwirizana ndi maganizo a Papa, ndipo maBishopi onsewa pamodzi ngati agwirizana kupereka uphunzitsi wowona pa za chikhulupiriro ndi umunthu. Ndipo payenera kukhala chigwirizano chopanda kukaika pa mfundo zomwe amanga limodzi. ’
Lumen Gentium § 25b.

Pali mfundo zisanu zoyeneretsa chigwirizanochi:

 1. Mgwirizano wa Bungwe la ma Bishopi.
  Mzachidzikire kuti ma Bishopi wonsewa ayenera kukhala wovomereka pa uphunzitsi wa za mpingo ngati gulu logwirizana.
 2. Monga ‘aweruzi’.
  Ma Bishopi ayenera kuperka maganizo awo a mumtima mwaufulu ndi mopanda mantha.
 3. Monga atumiki a Mpingo wonse.
  Ma Bishopiwa ayenera kumvvera mau a Mulungu womwe 'Mzimu Woyera akuwauza mitima mwawo’.
 4. Mogwirizana ndi chikhulupiriro ndi malamulo.
  chiphunzitso choterechi chimayenera kupherezera mu mfundo za chikhulupiriro chathu.
 5. Kudzera mu chimphunzitso chomwe popanda kupeneka aganizira bwino kuti ndi 'chiphunzitso choonadi.'
  Ndipo ma Bishopuwo mu mtima mwawo adziwe kuti ndi udindo wawo kutsutsa chiphunzitso chomwe chili ndi zopeneketsa.

Tikaunika pa nkhani ya unsembe wa amayi tiwona kuti nkhanii yatsekedwa mosatsatira dongosolo limeneli!

“Inu ma Bishopi mwavomereza magazizo ndi Kadinolo Ratzinger?!

Maganizo amenewa mwawatenga pa maphunzitso ati mu mpingo wathu?!”

“Akatswiri akuluakulu pa zophunzira za Mulungu akutsutsana ndi a Kadinolo Ratzinger pa zoletsa nkhani kupitiriza kukambirana nkhani ya unsembe wa amayi.
.

 1. Sukulu yaikulu ya maphunziro a unsembe ku Amereka
 2. Nicholas Lash, professor of divinity, Cambridge University, UK
 3. Francis A. Sullivan SJ, emeritus professor Gregorian University Rome
 4. Elizabeth A. Johnson, C.S.J., professor of theology at Fordham University, New York
 5. Gisbert Greshake, professor of theology at the University of Freiburg, Germany
 6. Ann O'Hara Graff, professor of theology at Seattle University, Washington
 7. Peter Hünermann, professor of theology at Tübingen University, Germany
 8. Sidney Cornelia Callahan, pastoral theologian, USA
 9. David Knight, pastoral theologian, Memphis, USA
 10. Richard Gaillardetz, associate professor, University of St. Thomas, Houseton, USA
 11. Klaus Nientiedt, ‘How Binding? “Ordinatio sacerdotalis” unleashes debate on the Magisterium’, Herder Korrespondenz 9 (1996) pp. 461-466.
 12. John H. Wright, ‘That all doubt may be removed’, America 171 (July 30-Aug. 6, 1994) pp. 16-19.
 13. Fr. Joseph Moingt SJ, editor of Recherches de Science Religieuse.
 14. Hugh O'Regan, editor of the on-line magazine, San Fransico Bay Catholic.
 15. The commission on "Woman and the Church" of the Belgian Bishops' Conference

Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi uphunzitsi wa mpingo wa mtsankho Mafunso apafupipafupi Zina?
kusintha kwa chikalidwe mfundo mbiri kumvera kwenikweni nthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi? uphunzitsi wosatsutsika? kudalilika? kumvera? kederera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mtchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?

Kodi tingaikenso chikhulupiriro chathu mwa a Phunzitsi a Mpingo?

Kodi tingaikenso chikhulupiriro chathu mwa a Phunzitsi a Mpingo?

“Malakhulidwe anu, akuchepetsa chikhulupiro changa mwa bamphunzitsi a Mpingo!

Popeza kuti a Mpunzitsi ena a Mpingo akhala akuganiaza molakwika pa zambiri m’mbuyomu, tingadzakhalenso bwanji ndi chikhulupiriro mwa a Phunzitsiwa.!?”

“Mzoonadi!

A Mphunzitsi a Mpingo ali ndi udindo wofunika mu Tchalitchi. Titha kufananitsa ndi udindo wa mabungwe woyanira zakudya ndi umoyo wa anthu womwe ali ndi ntchito yowonetsetsa kuti anthu akahale ndi umoyo wa ngwiro ndi thanzi.

Choncho sisikutithandiza mu Mpingo wathu tikamaona kuti a Khristu akutaya ayamba kupeneka mu chikhulipirio chomwe amayika pa atsogoleri a Mpingo, izi zikuchiku chifukwa a Phunzitsi Mpingo anataya, ndipo adakatayiratayira kudalilika kwawo pa za uphunzitsi.

Tchalitchi chathu chisamaiwale mau a Khristu amene amakamba za mchere womwe wataya kukoma kwake.

“Mchere wotaya kukma kwake?

Mukutanthauzanji?”

“Kuti anthu akhalenso pa chiphunzitso cha Mpingo, ku Vatican, likulu la Mpingo liyenera kulekeratu zizolowezi zosathandiza monga:

 • Kutsekereza Bungwe la ma Bishopi pa pomwe ali kumbirana mwaufulu wawo pankhani za Mpingo.
  Sinodi ya ma Bishopi inayambika ndi mfundo za pa nsonkhano wachiwiri wa Vatikani kuti mabishopi akahlenso ndi mphmvu zounikanso mfundo za Khanso yayikulu yotchedwa 'Curia'.
 • Kulowerera pomwe ma Bungwe a aBishopi akugwira ntchito za udindo wawo mwadongosolo.
  Tikudziwanso kuti ma Bishopi si akazembe a aPapa koma ndi akazembe a Khristu, choncho ayenera kugwira nchito yawo ya ukazembe popanda kusokonedwa ndi akulikulu ku Vatikani.
 • Kusankha anthu amantha omwe satsutsa zolakwika za kulikulu kuti akhale a Bishopi, nthumwi za ku mabungwe a akatswiri ophunzira za Mulungu ndi anthu ena kuti alowe m'maudindo ofunika mu Mpingo.
  Zimenezi zimapangitsa kuti Tchalitchi likhale ndi atsogoleri amene sangathe kutsata maganizo awo abwino mopanda mantha, koma omwe amangovomereza zomwe akulu ena akuwauza.
 • Kupondereza akatswiri ophunzira ntchito za Mulungu omwe amatsutsa atsogoleri akulu akapereka maganizo olakwika.
  Kuponnderezana kotereku kukupha luntha la atsogoleri ambiri ameme amaganiza mwanzeru, mozama komanso mopanda chinyengo.”
Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi a Phunzitsi a Mpingo Mafunso apafupipafupi Zina?
Kusintha kwa chikhalidwe mfundo mbiri kumvera kwenikweni mnthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi? uphunzitsi wa mpingo wosatsutsika? kudalilika? kumvera? kuderera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mu Tchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?

Kumvera mwa khungu?

Kumvera mwa khungu?

“Tisamongoti poti a Papa ndi a Papa!

Tchalitchi chimatiphunzitsa kumvera mopanda kukayika: ‘Mtima womvera ndi chifuniro ndi khalidwe lolemeka akulu. Komabe pauphunzitsi wokhudza zakumvera mchikhristu payenera kukhala umboni wokewanira kuti ndi uphunzitsi wowona wochokera kwa a Papa, angakhalenso pomwe a Papawo

sakukamba mfundo zomwe mzosatsutsika chifuka cha mphamvu zomwe a Papa alinazo mu u udindo wawo ngati Papa;izi zikutznthauza kuti, pomwe a Papa akupereka phunziro anthu aenera kumadzionera okha kutidi ndi uphunzitsa wowona, ndipo anthu adzitha kutsatiza mwaulemu ndipo zizikhala zotsogozedwa ndi mphatso za luntha zomwe a Papa amalandira kuchokera kwa Mzimu Woyera.”
Lumen Gentium, § 25c.

“Nkhaniyi siipherezera pano!

Kulemekeza akulu ndi kumvera kwenikweni sikusowa kuti tiphe chikumbumtima, tisakhale ndi nthumanzi kapenenso kuti tisatsate zomwe tikudziwa mosapeneka kuti ndi zoona!

Nsonkhano wa Khansolo yachiwiri ku Vatikani umatiphunzitsa kuti:: ‘Akulu wolamulira adzichita nthumanzi potsatira malamulo ndiponso pogwira ntchito ya utsogoleri.atiphunzitsanso kuti atsogeleri adzigwiritsa ntchito molinganga ndi luntha ndi maganizo awo, ndiponso pogwiritsa ntchto mphatso zawo zachilengedwe ndi zi zomwe amalandira kuchokera kwa Mzimu Woyera.’

Ndi m'njira yokhayi, Khansoliyi idatero, momwe kumvera sikuchotsa ulemu wa umunthu wa anthu woganiza bwino. Kumvera mu m'njira imeyi kumakuza kukhwima maganizo ndi ufulu zomwe ndi mphatso zoyenerera ana a Mulungu.
Perfectae Caritatis § 14.

“Kodi mwaiwala uphunzitsi wapamwa wa a Iginasiyo Woyera wa kuLoyola?

Iye adati, kumvera mwakhungu, kumatisandutsa ngati mtengo wakufa womwe ena amasandutsa ndodo yoyendera.

Kumvera moona kumatipangitsa kuti tivomereze kuti kanthumkoyera, ngakhale pa nthawi yomwe tikukawona kuti mkakuda!”

“Mzoonadi a Iginasio adatero. Komano awa anali mawu okuluwika. Sitingakainso, kodi sipaja iwowa ankafuna kuti atumiki a mchipani cha Majeziwiti, chipani chomwe iwo adaambitsa, kuti akhale anthu a mzeru, olungama ndipo a luntha pa zounikira maganizo osiyanasiyana?

Tanthauzo labwino la kumvera ndilo lomwe limalemekeza maganizo abwino aanthu potsatira maufulu awo ndipo mopanda mantha. Awa ndiye matanthauzo ena abwino a kumvera:

 • ‘Kumvera ndi kumvetsera chifuniro cha Mulungu mu mtima mwathu: ndi kutsatiza mopanda mantha nthumanzi ndi chikumbumtima chathu, monga chisomo chikutiunukira, ndiponso pomvetsera maganizo ma limana athu... choncho kumvera Khristu, kumvera a Bishopu athu, kumvera Mulungu — zonsezi magwero ake ali mu khumbo lofunitsitsa kukhala mwana wa Mulungu nchifanizo cha ufulu wa Mulungu.’
  Barbara Schmitz akuti
 • ‘Kumvera moona sikutanthauza kukhala okonzeka kutumikira ena nthawi zonse basi, komanso kuima patokha mosaopa pa maganizo ofunika ndi kuunikira bwino maganizo wena opanda pake amene angasokoneze maganizo athu angwiro’.
  Joan Chittister

Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi uphunzitsi wa mpingo wa mtsankho Mafunso apafupipafupi Zina?
kusintha kwa chikalidwe mfundo mbiri kumvera kwenikweni nthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi? uphunzitsi wosatsutsika? kudalilika? kumvera? kederera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mtchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?

Kuderera Atsogoleri?

Kuderera Atsogoleri?

“Ena akuti tikuderera a atsogoleri a Tchalitchi popereka maganizo athu atsutsa tsankho loretsa amayi kulowa unsembe!

akuti zomwe tikulembazi mzosokeneza athu wamba omwe sanazambe pa uphunzitsi wa Mpingo!

Suja Ambuye Yesu anati yemwe achita zochititsa manyazi pa gulu la ana amakwingiridwe chimwala chlemera m’khosi mwake ndipo aponyedwe mnyanja yozama!” (Matthew 18,6)

“Mungakhulupirire izi!

Anthu ambiri omwe amkalemekeza mafumu anaphedwa chifukwa cholimba mtima potsutsa zolakwika zina, nzachisoni kuti upandu woterewu umachitikanso mu Tchalitchi chathu.

pambuyo pa zonsezi Mpingo umadzionongera mbiri yake yabwino.”

“Tithana ndi onse wotsutsa!

Tikuti, dziwaponyani m'nyanja anthu otsutsa onsewo.

Kuti mpingo wathu upite patsogolo, tisawamvere chisoni anthu otsutsana nafe, tithane nawo basi!”

“Kumeneku ndiye kumanga Mpingo, eti?

Taimani mkukambire kankhani!

Pa Okotobala 22, 1707, mkulu wa gulu la ankhondo a panja ,Clowdesley Shovell, anabwere ku England pambuyo pa nkhondo omwe anamwnyana ndi amwaliwongo. Iwowa anali ndi sitima za pamanyanja zisanu pa nyanja ya Mediterranean.
Pa nthawi imeyeyo ma mkuti mayedwe ali wovutirapo ndiponso oowopsa. Kunja kudachita mkhungu choncho kunali kovuta kuloza kuti sitima zili patipati panyanja. komano pambuo pomfunsira a Kapitawo a sitima za nkhondo zisanuzo iwo adayamba ulendo wolowera ku m'mawa.
Koma m'modzi mwa asikikaliwo amene anali ndi mzeru za mayendedwe adawauza a Clowdesley kuti njira omwe atengao ndi oopsa.
Kutsutsana ndi maganizo a atsogoleri a mgulu la nkhondololi pa nthawiyo kunkatengedwa ngati upandu. Choncho msilikali yemwe adapereka maganizo osiyanawo adanyongedwa ndi kuphedwa nthawi yomweyo.
Komano ulendo wa sitimayo sudapite patali, popeza adagunda miyala yomwe inali nyanja ku kachilumba kotchedwa Scilly koma hali mbali yakumadzulo kwa England. Pangozii sitima zitatu zidathera pomwepo. askilikali ndi anthu oyendetsa sitima womwe chiwerengero chawo chidali choposa 2000 adafa pangoziyo, nawonso a Clowdesley Shovell adafa nawo pangoziyo.
Kodi pamenepa singati adanyonga wolakwika?

Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi uphunzitsi wa mpingo wa mtsankho Mafunso apafupipafupi Zina?
kusintha kwa chikalidwe mfundo mbiri kumvera kwenikweni nthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi? uphunzitsi wosatsutsika? kudalilika? kumvera? kederera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mtchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?

Ndi ati?! Maufulu a akhristu mu Tchalitchi?

Ndi ati?! Maufulu a akhristu mu Tchalitchi?

Tikayanira za mbiri ya Mpingo, Akatolika ambiri amaopa kukamba za ufulu wa akhristu mu tchalitchi chathu. Iwowa amaganiza kuti kukamba za ufulu wawo zitha kusiyana ndi maganizo a akukuluakulu kapenaso kuti kutereko mkusamvera Malamulo a Mulungu. Zoona zenizeni mzakuti pali zifukwa zomweka bwino zoti anthu athetse mantha amenewa ndi kuyamba kukambirana za ufulu weniweni wa akhristu.

Pano tinene mosabisa kuti tiri ndi maufulu, poyamba ngati anthu wolengenga ndi Mulungu ndiponso ngati mamembala a Tchalitchi.

*Ambuye Yesu anatipatsa mphamvuyosanduka ana a Mulungu (John 1,12). moga ana a amuna ndi a akazi,ndipo ngati athu wosankhidwa, tili ndi maufulu ambiri amene Mulungu anatipatsa (Romans 8,17).

* Ngakhalenso akuku a Mpingo mpaka lero kawirikawiri makamba za "maufulu" a mamembala a mpingo: pali ndime 26 mu Malamulo a Tchalitchi otchedwa Canon Law okamba za ufulu wa akhristu eniake. (can. 204 - 231).

* Thchalitchi lisowa kusintha mwachangu mu mfundo ndi njira zomwe athogoleri akuyendetsera mpingowu maka pa nkhani za ufulu wa anthu. Maufulu a akhristu, ansembe ndi mabishopi, amaene ndi mphtso zochekera kwa Mulungu akupondrezedwa mu dongosolo loyendetsera mpingo lomwe tilinalo panoli!

Choncho ife tikukupepha inu nonse awerengi athu kuku mutithandize polimbitsa We therefore urge our visitors to give full cooperation and allegiance to the Bungwe lokwenza ma "Ufulu a Akatolika mu Tchalitchi" (arccsites.org) Bungweli la lemba makala awiri omwe akupereka maganiozo ozama pa za ufulu wa akhristu:

 1. Charter of the Rights of the Catholics in the Church (arcc-catholic-rights.org/charter.htm)
 2. A Proposed Constitution of the Catholic Church (arcc-catholic-rights.org/constitution.htm)

Three afterthoughts:

1. Mtchalitchi cholemekekeza ,In a perfect Church, sitisowa kupondereza ufulu wa akhristu , monga mu ukwati wolemekeza nkhani ya 'maufulu' a bambo ndi mayi siikhal nkhani ya makangano.Komano, mongo BUngwe loyanira malamulo a Tchalitch limatiphunzitsa, Tchalitchi chathu "chimasowa kusintha" nthawi ndi nthawi. (Vatican II, Ecumenism § 6). Izinso nzofunuika kwambiri nthawi yathu ino pamene nkhanza za anthu ena amene ali ndi udindo mtchalitchi zikupangitsa kuti tchalitchi chathu chiwomeke nga 'banja losowa chilungamo ndi mtendere".

2. Timamva kawirikawiri ku ‘Mu Tchalitchi mulibe Demokalase’. Zinthu siziyenera kukhala choncho. Titha kunena kuti si Demokalase tialingalira kuti Mpingo udayambika mchifuniro cha ambuye yesu osati kubzolera mu voti ya wanthu. The Church is not a democracy in the sense that it was founded by the will of Christ, not by a plebiscite. Komano izi sizitanthuza kuti mu utsogoleri wa Mpingo uzisiyana ndi chifuniro cha anthu, Demokalase ndi njira yolamulira mpingo omwe igwirizana ndi chitukuko cha makono osati ulamuliro wachikale omwe mafumu paokha amamanga mfundo zoti athu wamba atsatitire..

3. Papa Paul VI anaitanitsa anthu kuti apange Bungwe lounikira Malamuro a Mpingo ndi kulemba Buku la malaumulo a Mpingo loti litsogoze a Khristu. Mzchisoni kuti pambuo pake maganizo oyamikikawa sanatsatidwe.

Chifukwa Chiyani tikutsutsana ndi uphunzitsi wa tsankho mu mpingo Mafunso a pafupipafupi
Kusintha kwa chikhalidwe mfundo mbiri kumvera koona nthumanzi pa chihkulupiriro
ufulu wa amayi? maphunzitso osatsutsika? kudalilika? kumvwera? kuderera?
Kodi 'maufulu a Katolika ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? _Ndemanga?

Was it JESUS who wanted women excluded from the priestly ministry?

Was it JESUS
who wanted women excluded
from the priestly ministry?

The Congregation for Doctrine in Rome

Congregation for Doctrine
in Rome

  “Jesus Christ did not call any woman to be part of the twelve apostles.”
Inter Insigniores § 9 – 12

“In this way Jesus established a permanent norm for the future Church: Jesus simply did not want women to be priests!”
Ordinatio Sacerdotalis

Background music?

Not so, not so!

Jesus wanted to liberate women. Excluding women permanently from the priesthood would be totally uncharacteristic of him. In fact, he made women equal partners in the priesthood which he imparted through baptism. This disposes women to share in his full priestly ministry.

  Jesus chose 12 apostles to replace the 12 tribal ‘fathers’ of Israel. In the cultural context of his time, it was natural he chose men for this limited purpose.

Moreover, it is invalid to argue from something Jesus did not do [= not choosing a woman on one occasion], to his establishing a permanent norm for all time to come.

And, do not forget, women were present at the Last Supper when Jesus said: “Do this in commemoration of me!”

Read: Suzanne Tunc and Marjorie Maguire.

 
  Last not least, Jesus made women his disciples who ministered in various ways. Women were called to be the first witnesses of his resurrection!!

Read Elisabeth Carroll.

Zina?

Further Readings!

Did Paul forbid women to teach?

Did Paul forbid women to teach?

“Paul excluded women from teaching and presiding in the assembly. Through this, he established a permanent norm – which excludes women from the priestly ministry. ”
Inter Insigniores § 9 – 12

“Paul distinguished between his female co-workers and male colleagues in the ministry. ”
Inter Insigniores

  The Congregation for Doctrine in Rome

Congregation for Doctrine
in Rome

Background music?

No need to blame Paul!

Yes, Paul imposed prohibitions on women which were inspired by local custom. For instance, he wanted them to wear a veil during prayer sessions:
1 Corinthians 11,2-16.


In such texts Paul sometimes ‘rationalised’, that is: he used popular arguments that do not contain doctrinal teaching.

  Christ’s ministerial priesthood derives from us becoming his priests through baptism.

Well, Paul taught the fundamental equality of men and women in Christ through baptism: Galatians 3,27-28.

It is true that some disciples of Paul forbade women to teach. But this was only to meet the specific needs of their community. The prohibition does not apply to the whole future Church as a permanent norm.

Read: 1 Timothy 2,1-12 and 1 Corinthians14,34-35 .

 
  No valid distinction can be made between two alleged categories among Paul’s co-workers: those in true ministries and those not. And Paul clearly counted women among his co-workers.

Read: Bernadette Brooten.

Scripture texts can mislead if we do not understand them properly.

Zina?

The ordination of women belongs to the type of ‘doctrine’ liable to distortion by cultural perceptions

The ordination of women belongs to the type of ‘doctrine’
liable to distortion
by cultural perceptions

Throughout the centuries, the formulation of Christian doctrine has been influenced by the prevailing culture of the time. Culture shift has affected even core doctrines such as those regarding the Trinity, the Incarnation, etc. But the ‘doctrines on the margin’ have often been totally hijacked by dominant cultures.

  • social order — democracy was forbidden, kings were thought to rule ‘by divine right’, the class system was upheld in church, colonialism was endorsed by popes.
  • the created world — Galileo was condemned as a heretic (!) for believing the earth goes round the sun, astrology was honoured, the six-day creation taught as inspired teaching.
  • liturgy — Roman everyday dress became ‘sacred vestments’, bishops were treated as feudal lords, Latin was considered God’s own language.
  • sexuality — Gnostic fears led to a negative approach, Roman & German civil laws shaped church wedding rules.

Women were excluded from exercising priestly functions on cultural grounds.

Women were considered ‘beautiful creatures’, but totally inferior to men.

  • less intelligent
  • emotionally unstable
  • unreliable
  • not capable of exercising any real leadership

This inferiority was seen confirmed by the view that women were not complete human beings.

Since the function of the female ovum was unknown, procreation was ascribed to the male sperm which alone, it was thought, contains new life.

This was the reason why theologians like Thomas Aquinas ruled out ordaining women.

Women also suffered from a terrible ‘malady’, namely their monthly periods. This made them unsuitable for service at God’s holy altar.

Menstrual fluid was held to be dirty, awful and even dangerous for others who touched it. The taboo was strong in the Roman world and prevailed through the Middle Ages until the 20th century.

Women were stopped from entering church during their periods or from receiving holy communion. At times they received communion on a cloth spread out over their hands. They certainly were too ‘unclean’ to approach the altar!

To cap it all, women were held responsible for causing men to sin.

Eve was blamed for seducing Adam, and all women were deemed to suffer the punishment of God’s curse on Eve, namely that she would always be subject to men.

It was cultural prejudices that propped up the exclusion of women from the priestly ministry. Church authorities have simply not woken up to this fact.

Mchifukwa chiyani tikutsutsana ndi uphunzitsi wa mpingo wa mtsankho Mafunso apafupipafupi Zina?
kusintha kwa chikalidwe mfundo mbiri kumvera kwenikweni nthumanzi ya chikhulupiriro
ufulu wokhala mayi? uphunzitsi wosatsutsika? kudalilika? kumvera? kederera?
Kodi ‘maufulu’ a aKatolika mtchalitchi ndi ati?
Muli ndi mafunso? __Maganizo ena? __Ndemanga?


Mpingo watidi ‘Ayi!’ – ndipo Ayi mpaka muyaya?

Mpingo watidi ‘Ayi!’
– ndipo Ayi mpaka muyaya?

“Zoti amayi asamadzodzedwe unsembe zinakahzikitsidwa ngati uphunzitsi wosatsutsika ndi a Phunzitsi akulu mu Mpingo.”

Ordinatio Sacerdotalis § 4

The Congregation for Doctrine in Rome

Bungwe la a Phunzitsi a za aMpingo ku Roma

“Mpingo ulibe mphamvu yodzodza amayi unsembe ndipo a khristu onse mu mpingo wathu agwirizane ndi chiphunzitso chimenechi mopanda kung’ung’udza.”

Inter Insigniores § 5

Background music?

Maphunzitso a akulu a Mpingo amatanthauza maphunsitso a mabishopi onse a chikalolika limodzi mu m’ziko lonse lapansi..

Uphunsitsi uamasanduka osastutsiaka pokhapohka ngati:
1. 1. pali chigwiriza pa mfundo za kukambiranna kwa ma Bishopi onse a mu mpingo
2. pomwe ma Bishopi avala udindongati aweruzi
3. pambuyo pomwetsera maganizo am a aKhristu
4. molinganizana ndi mphatso za chikhulupiriro poperekedwa ndi Mzimu woyera kapena chilungamo
5.akafika pogamula awa amakhala mathero okambirana nkhani yomwe imawunikidwayo.

Palibe mfundo ndi imodzi omwe ya chilinganizo chimechi ome inatsatidwa moyenera pogamula zoti amayi asamadzodzedwe unsembe.

Zokmirana zatsekedwa?
Ife tikuti ayi!

Ichi nchifukwa chake a katswiri wophunzira za Mulungu akutsutsa maphunzitso woletsa kukambiranabe nkhani ya unsembe wa amayi.

Poonjezera apo, kuti maphunziro a mpingo akhale woyenera, mayera kuvomerezedwa di a Khristu eni ake. . . izi siziri choncho popeza a aKatolika ambiri akutsutsa tsankho lotchingiriza amayi kulowa unsembe!

werengani: ‘Kulandira Uphunbzitsi wa Mpingo: Kuona Mwatsopano’ by Richard Gaillardetz.

Tiyeni titengerepo phunziro pa zomwe zidachitika m’buyomu.

Aka si koyamba kuti akuluakulu wophunzitsa za mpingo, ngakhale a Papa ambiri, anaperewera maganizo, poweruza molakwika nkhani zofunika kwambiri.

Bishopu Raymond A. Lucker posachedwa wapeza mfundo zoposa 65 pa maphunzitso olakwika a mpingo omwe pa kanthawi ankatengedwa ngati maphunzitso owona ndipo osatsutsika pano mpingo unakonza molondola mfundo zolakwikazi!

Mfundo zonsezi zikusonetsa poyera kuti yankho lenileni pa nkhani ya unsembe wa amayi silinapezeke popeza nkhaniyi yaletsedwa tisadafike pa mathero enieni choncho nkhanyi idakalipo! Return to opening menu?

Ndani angadziwe mosapeneka
uphunzitsi wowona wa Mpingo?

Werengani mafunso a kawirikawiri!

Can women not act in the person of Christ?

Can women not act
in the person of Christ?

Background music?

The Congregation for Doctrine in Rome

Congregation for Doctrine
in Rome

“The priest acts ‘in the person of Christ’. Since Jesus was a man, only a male priest can signify Christ at the Eucharist.”
Inter Insigniores § 24-28

“A sacrament is a sign . . . and the priest is a sign of Christ. Since it is not possible for the female sex to signify eminence of degree, for a woman is in the state of subjection, it follows that she cannot receive the sacrament of Order . . .”
Summa Theologica Suppl. qu. 39 art. 1.

Background music?

Oh dear, oh dear, oh dear!

This prejudice derives from the Fathers of the Church and theologians in the Middle Ages.

They attributed procreation to the father: the whole future child is carried in the male sperm, they thought; the mother is just like soil in which the seed grows up.

Since women are thus not complete human beings, they cannot represent Christ who is perfect.

Moreover, surely when a priest acts in the person of Christ, the quality signified by him is not Christ’s maleness, but his role as mediator!

Christ can be represented by women as much as by men because women are equal in Christ.

Women too bear Christ’s image.

Moreover, women already act as ‘other Christs’ when they are ministers of baptism and marriage.

In fact, women reflect better Christ’s feminine traits

Last not least, women too can represent Christ’s love which is the essence of his priesthood!

The Church is wrong, therefore, to exclude women from the priestly ministry on the plea that they cannot represent Christ! Zina