A Papa ndi bungwe la ma Bishopu ali ndi udindo wofunika kwambiri pounikira mfundo za chikhulipiriro chathu ndi chikhalidwe cha umunthu kudzera m’phamvu za uphunzitsi zomwe alinazo. Mphamvu za atsogolerizi zimakhala ndi tanthauzo zikadzera nchifuniro cha anthu onse osati a Papa pa okha
Mu nsokhano wachiwiri waukulu ku Vatikani, padali maganizo osinthan nfundo za mphamvu zomwe a Papa alinazo pa zogamula pamene pali chipeneko kuti mphamvu zimenezo zizilimbikitsa chifuro cha a Kristu one. Nzokhumudwitsa kuti maganizowa anakanidwa. Vatican II, Acta synodalia III/1, pp. 198-199; R.R.Gaillardetz, Teaching with Authority. A Theology of the Magisterium in the Church, Liturgical Press 1997, p. 154.
“Mpingo Ekelezia wonse pamodzi, monga anthu odzodzedwa ndi Mzimu Woyera (1 Yohane 2, 20.27, sungathe Kulawa pa nkhani za chipembedzo.”Vatican II, Lumen Gentium, § 12 | “anthu A Mulungu amatsatira chikhulupiriro chawo mopanda kutsaliza akatsogozedwa ndi anthu Woyera, izi zimazama ndi mzeru zoona, ndipo zimagwirizana ndi moyo wa chiKhristu.Vatican II, Lumen Gentium, § 12 | “Tithokoze ku mphatso za uzimu zodabwitsa zimene zimaoneka kudzera m’moyo mwa a Papa ndipo zimeme zimaonetsa ubwino wa moyo wachikhristu, izi zimaphera mphongo mphatso ya Mpingo wa Eklezia zomwe zimapangitsa kuti a Kriastsu pamodzi ndi a tsogoleli awo sangathe kulakwa pa nkhani za chi khulupiriro."Vatican II, Lumen Gentium, § 12 |
Kafufuku akusonyeza kuti Akatolika enieni a m’maiko ambiri akhulupira kuti amayinso ngoitanidwa ku unsembe.M’musimu tasindikiza ma peresenti a zotsatira za kafukufuyu. Zimemzi zisonyesa unyinji wa Akatolika omwe amafuna unsembe wa Amayi |
![]() | ![]() | ![]() | ![]() | ![]() | ![]() | ![]() | ![]() | ![]() | ![]() |
| Great Britain | Canada | Spain | Portugal | Netherlands | Germany | Italy | Australia | Ireland | USA |
| 65% | 66% | 74% | 71% | 86% | 71% | 58% | 62% | 67% | 68% |
Mkhaniyi ya kambidwa mwa tsatanetsatane mu buku ili: Mfundo za uphunzitsi wa mpingo si zisamamangike ndi voti, kapensa maganizo a unyinjiZotsatra za kafukufukku ali pamwambu zikusonyeza kuti, aKatolika ambiri, omwe amatsata chikhulupiro cha Mpingo mwa khama komanso motsatira bwino maphunziro a Mpingo, akuganiza kuti palibe zikukwa zenizeni zoletsa amayi kudzodzedwa unsembe. Akatolika amenewa nawonso ali mu gawo la Ekeleziya amene pamodzi ndi okhulupirira onse sangathe kulakwa pa nkhani ya chikhulupiro chathu. |
“Kodi pamenepa tingati tikuderera Akuluakulu a Mpingo?”












